-
Ekisodo 7:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako, utambasule dzanja lako nʼkuloza madzi a mu Iguputo.+ Uloze mitsinje yawo, ngalande zawo,* zithaphwi zawo+ ndi malo onse amene amasungira madzi kuti asanduke magazi.’ Choncho madzi amʼdziko lonse la Iguputo, ngakhalenso madzi amʼmitsuko yawo yamtengo ndi yamwala adzakhala magazi.”
-