Ekisodo 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova anachitadi zimenezi, moti ntchentche zoluma zinali paliponse mʼnyumba ya Farao, mʼnyumba za atumiki ake ndi mʼdziko lonse la Iguputo.+ Ntchentchezo+ zinabweretsa mavuto aakulu kwa anthu a ku Iguputo.
24 Yehova anachitadi zimenezi, moti ntchentche zoluma zinali paliponse mʼnyumba ya Farao, mʼnyumba za atumiki ake ndi mʼdziko lonse la Iguputo.+ Ntchentchezo+ zinabweretsa mavuto aakulu kwa anthu a ku Iguputo.