Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala ndi moto* padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala mʼdziko la Iguputo.
23 Ndiyeno Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala ndi moto* padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala mʼdziko la Iguputo.