Ekisodo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzawabweretsa nʼkuwakhazikitsa mʼphiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukhalemo, inu Yehova.Malo opatulika amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.
17 Mudzawabweretsa nʼkuwakhazikitsa mʼphiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukhalemo, inu Yehova.Malo opatulika amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.