-
Ezekieli 20:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ine ndinawalowetsa mʼdziko limene ndinalumbira kuti ndidzawapatsa.+ Koma ataona mapiri onse ataliatali ndi mitengo ya masamba ambiri,+ anayamba kupereka nsembe zawo ndi zopereka zawo zimene sizinkandisangalatsa. Anapereka kafungo kosangalatsa* ka nsembe zawo ndiponso kuthira nsembe zawo zachakumwa pamalo amenewo.
-