Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+ 1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso Likasa la Mulungu linalandidwa, ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana a Eli, anaphedwa.+
18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+