1 Samueli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja la Yehova linayamba kukhaulitsa anthu a ku Asidodi, ndipo linachititsa kuti anthu amumzinda wa Asidodi komanso madera ake ozungulira ayambe kudwala matenda a mudzi.*+
6 Dzanja la Yehova linayamba kukhaulitsa anthu a ku Asidodi, ndipo linachititsa kuti anthu amumzinda wa Asidodi komanso madera ake ozungulira ayambe kudwala matenda a mudzi.*+