-
1 Samueli 16:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Iye anatumadi munthu kukamʼtenga. Mnyamatayo anali wa maso okongola ndiponso wooneka bwino.+ Ndiyeno Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+ 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+
-