2 Samueli 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Davide anauza Mikala kuti: “Inetu pamene paja ndimasangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha mʼmalo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse kuti ndikhale mtsogoleri wa anthu a Yehova, Aisiraeli.+ Choncho ndidzasangalala pamaso pa Yehova.
21 Davide anauza Mikala kuti: “Inetu pamene paja ndimasangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha mʼmalo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse kuti ndikhale mtsogoleri wa anthu a Yehova, Aisiraeli.+ Choncho ndidzasangalala pamaso pa Yehova.