Yesaya 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzapita kunkhondo ngati munthu wamphamvu.+ Iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri ngati msilikali.+ Adzafuula, inde adzafuula ngati anthu amene akupita kunkhondo.Iye adzasonyeza kuti ndi wamphamvu kwambiri kuposa adani ake.+
13 Yehova adzapita kunkhondo ngati munthu wamphamvu.+ Iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri ngati msilikali.+ Adzafuula, inde adzafuula ngati anthu amene akupita kunkhondo.Iye adzasonyeza kuti ndi wamphamvu kwambiri kuposa adani ake.+