Ekisodo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukauze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+ Yesaya 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova amene anandipanga ndili mʼmimba kuti ndikhale mtumiki wake,Wandiuza kuti nditenge Yakobo nʼkumubwezera kwa iye,Nʼcholinga choti Isiraeli asonkhanitsidwe kwa iye.+ Ine ndidzalemekezedwa pamaso pa YehovaNdipo Mulungu wanga adzakhala mphamvu yanga.
22 Ukauze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+
5 Ndiyeno Yehova amene anandipanga ndili mʼmimba kuti ndikhale mtumiki wake,Wandiuza kuti nditenge Yakobo nʼkumubwezera kwa iye,Nʼcholinga choti Isiraeli asonkhanitsidwe kwa iye.+ Ine ndidzalemekezedwa pamaso pa YehovaNdipo Mulungu wanga adzakhala mphamvu yanga.