Chivumbulutso 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mkaziyo anabereka mwana wamwamuna,+ mnyamata amene adzakusa mitundu yonse ya anthu ndi ndodo yachitsulo.+ Ndipo mwana wakeyo anatengedwa msangamsanga nʼkupititsidwa kwa Mulungu ndi kumpando wake wachifumu. Chivumbulutso 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+
5 Mkaziyo anabereka mwana wamwamuna,+ mnyamata amene adzakusa mitundu yonse ya anthu ndi ndodo yachitsulo.+ Ndipo mwana wakeyo anatengedwa msangamsanga nʼkupititsidwa kwa Mulungu ndi kumpando wake wachifumu.
15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+