Yesaya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.
13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.