Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo.
6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo.