Deuteronomo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.
24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.