Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+ Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa anthu achilendo andiukira,Ndipo anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga.+ Iwo salemekeza Mulungu.*+ (Selah)
4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+
3 Chifukwa anthu achilendo andiukira,Ndipo anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga.+ Iwo salemekeza Mulungu.*+ (Selah)