1 Timoteyo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndi wachimwemwe ndi Wamphamvu komanso ndi Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye,+ ndipo adzaonekera pa nthawi yake. Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+ Chivumbulutso 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+
15 Iye ndi wachimwemwe ndi Wamphamvu komanso ndi Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye,+ ndipo adzaonekera pa nthawi yake.
5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+
16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+