Miyambo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu amene amanyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,Koma wosangalala ndi munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+ Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamabwezere choipa pa choipa.+ Muziganizira zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.
21 Munthu amene amanyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,Koma wosangalala ndi munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+