-
Salimo 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kodi palibe aliyense womvetsa zinthu pakati pa anthu ochita zoipawa?
Iwo amadya anthu anga ngati kuti akudya chakudya.
Ndipo sapemphera kwa Yehova.
-