1 Mbiri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
26 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+