Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Simungachite zimenezo, simungaphe munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama alangidwe limodzi ndi woipa.+ Simungachite zimenezo.+ Ndinu Woweruza wa dziko lonse lapansi. Ndiye kodi simuchita chilungamo?”+

  • Salimo 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo.+

      Adzapereka zigamulo zolungama pa milandu ya mitundu ya anthu.+

  • Salimo 98:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pamaso pa Yehova chifukwa iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi.

      Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+

      Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.+

  • Machitidwe 17:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+

  • 2 Petulo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma ndi mawu a Mulungu omwewo, kumwamba ndi dziko lapansi zimene zilipo panopa, azisungira moto ndipo akuzisungabe mpaka pa tsiku limene adzaweruze komanso kuwononga anthu osaopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena