Yohane 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amene amakhulupirira Mwanayo adzalandira moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzalandira moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu udzakhalabe pa iye.+
36 Amene amakhulupirira Mwanayo adzalandira moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzalandira moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu udzakhalabe pa iye.+