Yesaya 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aponya milungu yawo pamoto,+ chifukwa sinali milungu, koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala. Nʼchifukwa chake anatha kuiwononga.
19 Aponya milungu yawo pamoto,+ chifukwa sinali milungu, koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala. Nʼchifukwa chake anatha kuiwononga.