8 Musachite mantha,
Ndipo musathedwe nzeru chifukwa cha mantha.+
Kodi sindinauziretu aliyense wa inu ndi kulengeza zimenezi?
Inu ndinu mboni zanga.+
Kodi palinso Mulungu wina kupatulapo ine?
Ayi, palibe Thanthwe lina.+ Palibe lina limene ndikulidziwa.’”