Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, ndi lamphamvu zochuluka.+

      Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.

  • Yesaya 52:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova waika poyera dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione.+

      Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona zimene Mulungu wathu wachita potipulumutsa.*+

  • Yesaya 59:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti nʼkuthandizapo,

      Anadabwa kwambiri kuti palibe amene akulowererapo.

      Choncho anapulumutsa anthu* ndi dzanja lake,

      Ndipo chilungamo chake nʼchimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.

  • Yesaya 63:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndinayangʼana koma panalibe wondithandiza.

      Ndinadabwa kuti palibe amene anandithandiza.

      Choncho dzanja langa linandibweretsera chipulumutso,*+

      Ndipo mkwiyo wanga ndi umene unandithandiza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena