Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 95:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Bwerani, tiyeni timulambire komanso kumugwadira.

      Tiyeni tigwade pamaso pa Yehova amene anatipanga.+

       7 Chifukwa iye ndi Mulungu wathu

      Ndipo ife ndi anthu amene iye akuweta,

      Nkhosa zimene akuzisamalira.*+

      Lero anthu inu mukamvera mawu ake,+

  • Ezekieli 34:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 ‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu basi ndipo ine ndine Mulungu wanu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”

  • 1 Petulo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Poyamba munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa mʼbusa wanu+ ndi woyangʼanira miyoyo yanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena