Yesaya 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+Ndipo mafumu+ adzatsata ulemerero wako wonyezimira.*+ Zekariya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu idzabwera kudzafunafuna Yehova wa magulu ankhondo akumwamba mu Yerusalemu,+ ndiponso kudzapempha Yehova kuti awakomere mtima.’*
22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu idzabwera kudzafunafuna Yehova wa magulu ankhondo akumwamba mu Yerusalemu,+ ndiponso kudzapempha Yehova kuti awakomere mtima.’*