Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwa

      Chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+

      Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu,

      Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”*

  • Miyambo 22:22, 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+

      Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+

      23 Chifukwa Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+

      Ndipo adzachotsa moyo wa anthu amene akuwabera mwachinyengo.

  • Yakobo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena