Ekisodo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkukamanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, mʼmunsi mwa phiri. Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”
4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkukamanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, mʼmunsi mwa phiri.
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”