Nehemiya 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+
31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+