Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 78:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Koma ankawamvera chifundo.+

      Ankawakhululukira* machimo awo ndipo sankawawononga.+

      Nthawi zambiri ankabweza mkwiyo wake+

      Mʼmalo moonetsa ukali wake wonse.

  • Yesaya 49:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa

      Kapena kulephera kuchitira chifundo mwana wochokera mʼmimba mwake?

      Ngakhale amayi amenewa ataiwala, ine sindingakuiwale.+

  • Malaki 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Iwo adzakhala anthu anga,+ pa tsiku limene ndidzawasandutse chuma chapadera,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ndidzawachitira chifundo ngati mmene munthu amachitira chifundo mwana wake amene amamutumikira.+

  • Yakobo 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa munthu amene akudwalayo* ndipo Yehova* adzamulimbitsa. Komanso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena