2 Mafumu 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+ Luka 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mngeloyo anamuyankha kuti: “Ine ndine Gabirieli+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu+ ndipo wandituma kudzalankhula nawe komanso kudzalengeza uthenga wabwinowu kwa iwe.
35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+
19 Mngeloyo anamuyankha kuti: “Ine ndine Gabirieli+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu+ ndipo wandituma kudzalankhula nawe komanso kudzalengeza uthenga wabwinowu kwa iwe.