2 Samueli 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anakwera pakerubi+ ndipo anabwera akuuluka. Anaonekera pamapiko a mngelo.*+ Yobu 38:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yehova anayankha Yobu kudzera mumphepo yamkuntho kuti:+