Yobu 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu wa Mulungu unandiumba,+Ndipo mpweya wa Wamphamvuyonse unandipatsa moyo.+ Machitidwe 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Paja chifukwa cha iye tili ndi moyo, timayenda ndipo tilipo, ngati mmene andakatulo anu ena ananenera kuti, ‘Paja ndife ana ake.’*
28 Paja chifukwa cha iye tili ndi moyo, timayenda ndipo tilipo, ngati mmene andakatulo anu ena ananenera kuti, ‘Paja ndife ana ake.’*