Salimo 18:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mumakulitsa njira kuti mapazi anga azidutsamo,Ndipo mapazi anga sadzaterereka.+ Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+ Salimo 119:133 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Nditsogolereni ndi mawu anu kuti ndiyende mʼnjira yotetezeka.Musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sadzalola kuti phazi lako literereke.*+ Amene akukuyangʼanira sadzawodzera.
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+
133 Nditsogolereni ndi mawu anu kuti ndiyende mʼnjira yotetezeka.Musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+