Yesaya 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu, inu Yehova, muone.+ Imvani mawu onse amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.+
17 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu, inu Yehova, muone.+ Imvani mawu onse amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.+