Ekisodo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anachitadi zomwezo. Aroni anatambasula dzanja lake nʼkumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo tizilomboto tinayamba kusowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse lamʼdziko la Iguputo linasanduka tizilombo toyamwa magazi.+ Ekisodo 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova anachitadi zimenezi, moti ntchentche zoluma zinali paliponse mʼnyumba ya Farao, mʼnyumba za atumiki ake ndi mʼdziko lonse la Iguputo.+ Ntchentchezo+ zinabweretsa mavuto aakulu kwa anthu a ku Iguputo.
17 Iwo anachitadi zomwezo. Aroni anatambasula dzanja lake nʼkumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo tizilomboto tinayamba kusowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse lamʼdziko la Iguputo linasanduka tizilombo toyamwa magazi.+
24 Yehova anachitadi zimenezi, moti ntchentche zoluma zinali paliponse mʼnyumba ya Farao, mʼnyumba za atumiki ake ndi mʼdziko lonse la Iguputo.+ Ntchentchezo+ zinabweretsa mavuto aakulu kwa anthu a ku Iguputo.