Salimo 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova atamandike,Chifukwa mʼnjira yodabwitsa, wandisonyeza chikondi chokhulupirika+ mumzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+
21 Yehova atamandike,Chifukwa mʼnjira yodabwitsa, wandisonyeza chikondi chokhulupirika+ mumzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+
22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+