Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 (Chifukwa pali amuna ena amene akhala ansembe popanda lumbiro, koma ameneyu wakhala wansembe pochita kumulumbirira. Lumbiro limeneli ndi la amene ananena za wansembeyo kuti: “Yehova* walumbira kuti, ‘Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,’ ndipo sadzasintha maganizo.”)+

  • Aheberi 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ mpaka kalekale.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena