Mlaliki 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa munthu sadziwa nthawi imene tsoka lingamugwere.+ Mofanana ndi nsomba zimene zimagwidwa mu ukonde wakupha, komanso mbalame zimene zimagwidwa mumsampha, ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka, tsokalo likawagwera mwadzidzidzi.
12 Chifukwa munthu sadziwa nthawi imene tsoka lingamugwere.+ Mofanana ndi nsomba zimene zimagwidwa mu ukonde wakupha, komanso mbalame zimene zimagwidwa mumsampha, ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka, tsokalo likawagwera mwadzidzidzi.