Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+
4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+