Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pa nthawi ya mavuto, ndinaitana Yehova,+

      Ndinapitiriza kuitana Mulungu wanga.

      Iye anamva mawu anga ali mʼkachisi wake,

      Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+

  • Salimo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma inu Yehova mudzamva pempho la anthu ofatsa.+

      Mudzalimbitsa mitima yawo+ ndipo mudzawamvetsera mwatcheru.+

  • Salimo 34:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+

      Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena