Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.
99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.