Yesaya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira? Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pamenepa? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira?
6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+