2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova, chonde ndikukupemphani kuti mukumbukire kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse komanso ndachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri. Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.
3 “Yehova, chonde ndikukupemphani kuti mukumbukire kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse komanso ndachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.
25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.