Yesaya 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova ndikukupemphani kuti chonde, mukumbukire+ kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse+ komanso ndachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.
3 “Yehova ndikukupemphani kuti chonde, mukumbukire+ kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse+ komanso ndachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.