Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, uzitsatira malamulo a bambo ako,Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+ Miyambo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukamayenda adzakutsogolera.Ukamagona adzakulondera.Ndipo ukadzuka, adzakuuza zochita.*