Yeremiya 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+Mawu anu anakondweretsa komanso kusangalatsa mtima wanga,Chifukwa ine ndimatchedwa ndi dzina lanu, inu Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba.
16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+Mawu anu anakondweretsa komanso kusangalatsa mtima wanga,Chifukwa ine ndimatchedwa ndi dzina lanu, inu Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba.