Luka 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Khalani maso ndipo chenjerani ndi dyera* lamtundu uliwonse,+ chifukwa ngakhale munthu atakhala ndi zochuluka chotani, moyo wake suchokera mʼzinthu zimene ali nazo.”+ 1 Timoteyo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa kukonda ndalama kumayambitsa* zopweteka za mtundu uliwonse, ndipo chifukwa chotengeka ndi chikondi chimenechi, ena asiya chikhulupiriro ndipo adzibweretsera zopweteka zambiri pathupi lawo.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+
15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Khalani maso ndipo chenjerani ndi dyera* lamtundu uliwonse,+ chifukwa ngakhale munthu atakhala ndi zochuluka chotani, moyo wake suchokera mʼzinthu zimene ali nazo.”+
10 Chifukwa kukonda ndalama kumayambitsa* zopweteka za mtundu uliwonse, ndipo chifukwa chotengeka ndi chikondi chimenechi, ena asiya chikhulupiriro ndipo adzibweretsera zopweteka zambiri pathupi lawo.+
5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+