Ekisodo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anabwerera kwa Yehova nʼkukamuuza zimene anthuwo anayankha.
8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anabwerera kwa Yehova nʼkukamuuza zimene anthuwo anayankha.